Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 9:2 - Buku Lopatulika

2 Ngati sindili mtumwi kwa ena, komatu ndili kwa inu; pakuti chizindikiro cha utumwi wanga ndi inu mwa Ambuye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ngati sindili mtumwi kwa ena, komatu ndili kwa inu; pakuti chizindikiro cha utumwi wanga ndi inu mwa Ambuye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ngakhaletu ena sandiyesa mtumwi, koma kwa inu ndine mtumwi ndithu, pakuti moyo wanu wachikhristu ndi umboni wakuti ndinedi mtumwi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ngakhale kwa ena sindingakhale mtumwi, mosakayika ndine mtumwi kwa inu! Poti inu ndi chizindikiro cha utumwi wanga mwa Ambuye.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 9:2
6 Mawu Ofanana  

Iye amene analandira umboni wake anaikapo chizindikiro chake kuti Mulungu ali woona.


Gwirani ntchito si chifukwa cha chakudya chimene chitayika koma cha chakudya chimene chitsalira kumoyo wosatha, chimene Mwana wa Munthu adzakupatsani inu; pakuti ameneyo Atate, ndiye Mulungu, adamlembera chizindikiro.


alowe malo a utumiki uwu ndi utumwi, kuchokera komwe Yudasi anapatukira, kuti apite kumalo a iye yekha.


Chodzikanira changa kwa iwo amene andifunsa ine ndi ichi:


Zizindikirotu za mtumwi zinachitika pakati pa inu, m'chipiriro chonse, ndi zizindikiro, ndi zozizwa, ndi zamphamvu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa