1 Akorinto 8:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti ngakhalenso iliko yoti yonenedwa milungu, kapena m'mwamba, kapena padziko lapansi, monga iliko milungu yambiri, ndi ambuye ambiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti ngakhalenso iliko yoti yonenedwa milungu, kapena m'mwamba, kapena pa dziko lapansi, monga iliko milungu yambiri, ndi ambuye ambiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ena amati kuli zinthu zina kumwambaku, kapena pansi pano, zimene iwo amazitchula milungu, ndipo anthuwo ali nayodi milungu yambiri, ndi ambuye ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Popeza kuti ngakhale pali yotchedwa milungu, kaya ndi kumwamba kapena pa dziko lapansi (poti ilipodi milungu yambirimbiri ndi ambuye ambirimbiri), Onani mutuwo |