1 Akorinto 8:13 - Buku Lopatulika13 Chifukwa chake, ngati chakudya chikhumudwitsa mbale wanga, sindidzadya nyama kunthawi yonse, kuti ndingakhumudwitse mbale wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Chifukwa chake, ngati chakudya chikhumudwitsa mbale wanga, sindidzadya nyama kunthawi yonse, kuti ndingakhumudwitse mbale wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Nchifukwa chake, ngati chakudya chingaphunthwitse mbale wanga wachikhristu, sindidzadya konse nyama, kuti ndingamuphunthwitse mbale wangayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Nʼchifukwa chake ngati zimene ine ndimadya zichititsa mʼbale wanga kugwa mu tchimo, sindidzadyanso chakudyacho kuti mʼbaleyo ndisamuchimwitse. Onani mutuwo |