1 Akorinto 7:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo mkazi amene ali naye mwamuna wosakhulupirira, navomera mtima iye kukhala naye pamodzi, asalekane naye mwamunayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo mkazi amene ali naye mwamuna wosakhulupirira, navomera mtima iye kukhala naye pamodzi, asalekane naye mwamunayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Momwemonso ngati mkhristu wamkazi ali ndi mwamuna wachikunja, ndipo mwamunayo avomera kukhala naye, mkaziyo asathetse ukwatiwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ngati mayi wina ali ndi mwamuna wosakhulupirira ndipo mwamunayo walola kukhala pa banja ndi mayiyo, ameneyo asamuleke. Onani mutuwo |