1 Akorinto 6:8 - Buku Lopatulika8 Koma muipsa, nimunyenga, ndipo mutero nao abale anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma muipsa, nimunyenga, ndipo mutero nao abale anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma inuyo ndi amene mukulakwira ena, ndipo mukuŵabera, ngakhale iwowo ndi akhristu anzanu! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mʼmalo mwake, inuyo ndiye mumabera ena ndi kuwalakwira, ndipo mumachita izi kwa abale anu. Onani mutuwo |