1 Akorinto 6:6 - Buku Lopatulika6 koma mbale anena mlandu ndi mbale, ndikotu kwa osakhulupirira? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 koma mbale anena mlandu ndi mbale, ndikotu kwa osakhulupirira? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Bwanji mkhristu akuimba mlandu mkhristu mnzake, mlanduwo nkuupereka kwa anthu akunja kuti auzenge? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma mʼmalo mwake mʼbale atengera ku bwalo la mlandu mʼbale mnzake kukaweruzidwa. Zonsezi pamaso pa akunja! Onani mutuwo |