1 Akorinto 5:9 - Buku Lopatulika9 Ndinalembera inu m'kalata ija, kuti musayanjane ndi achigololo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndinalembera inu m'kalata uja, kuti musayanjane ndi achigololo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 M'kalata imene ndidaakulemberani, ndidaakuuzani kuti musamayanjane nawo anthu adama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndakulemberani mʼkalata yanga kuti musayanjane nawo anthu achigololo. Onani mutuwo |