1 Akorinto 4:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti sindidziwa kanthu kakundipalamulitsa; koma m'menemo sindiyesedwa wolungama; koma wondiweruza ine ndiye Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti sindidziwa kanthu kakundipalamulitsa; koma m'menemo sindiyesedwa wolungama; koma wondiweruza ine ndiye Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndilibe kanthu konditsutsa mumtima mwanga, komabe ngakhale chimenechi si chitsimikizo chakuti ndine wolungama. Ondiweruza ndi Ambuye basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Chikumbumtima changa sichikunditsutsa, koma sikuti ndine wolungama. Wondiweruza ine ndi Ambuye. Onani mutuwo |