1 Akorinto 3:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti pamene wina anena, Ine ndine wa Paulo; koma mnzake, Ndine wa Apolo; simuli anthu kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti pamene wina anena, Ine ndine wa Paulo; koma mnzake, Ndine wa Apolo; simuli anthu kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mumangoti ali apa, “Ine ndine wa Paulo,” ali apa, “Ine ndine wa Apolo.” Kodi mukamatero simukuchita ngati anthu odalira zapansipano? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pamene wina anena kuti, “Ine ndimatsatira Paulo,” ndipo wina akuti, “Ine ndimatsatira Apolo,” Kodi si inu akunja? Onani mutuwo |