1 Akorinto 3:14 - Buku Lopatulika14 Ngati ntchito ya munthu aliyense ikhala imene anaimangako, adzalandira mphotho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ngati ntchito ya munthu aliyense ikhala imene anaimangako, adzalandira mphotho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Zimene munthu adamanga pamazikopo zikadzakhalapobe, mwiniwakeyo adzalandira mphotho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ngati zimene zamangidwazo sizidzagwa, adzalandira mphotho yake. Onani mutuwo |