1 Akorinto 10:21 - Buku Lopatulika21 Simungathe kumwera chikho cha Ambuye, ndi chikho cha ziwanda; simungathe kulandirako kugome la Ambuye, ndi kugome la ziwanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Simungathe kumwera chikho cha Ambuye, ndi chikho cha ziwanda; simungathe kulandirako kugome la Ambuye, ndi kugome la ziwanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Simungathe kumwera m'chikho cha Ambuye nkumweranso m'chikho cha Satana. Simungathe kudyera pa tebulo la Ambuye nkudyeranso pa tebulo la Satana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Simungamwe chikho cha Ambuye, ndi kukamweranso chikho cha ziwanda. Simungadyere pa tebulo la Ambuye ndiponso la ziwanda. Onani mutuwo |