1 Akorinto 10:12 - Buku Lopatulika12 Chifukwa chake iye wakuyesa kuti ali chilili, ayang'anire kuti angagwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chifukwa chake iye wakuyesa kuti ali chilili, ayang'anire kuti angagwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono amene akuganiza kuti waimirira molimba, achenjere kuti angagwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Choncho, ngati mukuganiza kuti mwayima mwamphamvu, samalani mungagwe! Onani mutuwo |