1 Akorinto 1:9 - Buku Lopatulika9 Mulungu ali wokhulupirika amene munaitanidwa mwa Iye, ku chiyanjano cha Mwana wake Yesu Khristu, Ambuye wathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mulungu ali wokhulupirika amene munaitanidwa mwa Iye, ku chiyanjano cha Mwana wake Yesu Khristu, Ambuye wathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mulungu ndi wokhulupirika, ndipo Iye ndiye amene adakuitanani kuti mukhale a mtima umodzi ndi Mwana wake Yesu Khristu Ambuye athu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mulungu amene wakuyitanani inu mu chiyanjano ndi Mwana wake Yesu Khristu Ambuye athu ngokhulupirika. Onani mutuwo |