ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;
Numeri 7:52 - Buku Lopatulika tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo; |
ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;
ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa za mphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Elisama mwana wa Amihudi.