Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:52 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

52 mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

52 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

52 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

52 Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:52
2 Mawu Ofanana  

mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa imodzi yayimuna ndi mwana wankhosa wamwamuna mmodzi wa chaka chimodzi, nsembe yopsereza;


ngʼombe ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Elisama mwana wa Amihudi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa