Ataroti, ndi Diboni, ndi Yazere, ndi Nimira, ndi Hesiboni, ndi Eleyale, ndi Sibima, ndi Nebo, ndi Beoni,
Numeri 32:36 - Buku Lopatulika ndi Betenimura, ndi Beteharani: mizinda ya m'malinga, ndi makola a zoweta. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Betenimura, ndi Beteharani: midzi ya m'malinga, ndi makola a zoweta. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Betenimira ndi Beteharani. Yonseyo inali yozingidwa ndi malinga. Ndipo adamanganso makola a nkhosa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Beti-Nimira ndi Beti-Harani mizinda ya malinga. Anamanganso makola a ziweto zawo. |
Ataroti, ndi Diboni, ndi Yazere, ndi Nimira, ndi Hesiboni, ndi Eleyale, ndi Sibima, ndi Nebo, ndi Beoni,
ndipo m'chigwa Beteharamu, ndi Betenimura, ndi Sukoti, ndi Zafoni, chotsala cha ufumu wa Sihoni mfumu ya Hesiboni, Yordani ndi malire ake, mpaka malekezero a nyanja ya Kinereti, tsidya lija la Yordani kum'mawa.