Numeri 3:49 - Buku Lopatulika Pamenepo Mose analandira ndalama zoombola nazo kwa iwo akuposa aja adawaombola Alevi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo Mose analandira ndalama zoombola nazo kwa iwo akuposa aja adawaombola Alevi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho Mose adatenga ndalama zoombolera zija kwa Aisraele amene chiŵerengero chao chidapitirira chiŵerengero cha amene adaomboledwa ndi Alevi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho Mose anatenga ndalama zowombolera zija kuchokera kwa Aisraeli amene chiwerengero chawo chinaposa chiwerengero cha omwe anawomboledwa ndi Alevi. |
analandira ndalamazo kwa oyamba kubadwa a ana a Israele; masekeli chikwi chimodzi mphambu mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi mphambu asanu, kuyesa sekeli wa malo opatulika.