Numeri 27:15 - Buku Lopatulika Ndipo Mose ananena ndi Yehova, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose ananena ndi Yehova, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose adapempha Chauta kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mose anati kwa Yehova, |
popeza munapikisana nao mau anga m'chipululu cha Zini, potsutsana nane khamulo, osandipatula Ine pamadziwo pamaso pao. Ndiwo madzi a Meriba mu Kadesi, m'chipululu cha Zini.