Ndipo akapanda abale a atate wake, mupatse wa chibale wake woyandikizana naye wa fuko lake cholowa chake, likhale lakelake; ndipo likhale kwa ana a Israele lemba monga Yehova wamuuza Mose.
Numeri 27:10 - Buku Lopatulika Ndipo akapanda kukhala nao abale, mupatse abale a atate wake cholowa chake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo akapanda kukhala nao abale, mupatse abale a atate wake cholowa chake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Akakhala kuti alibe abale, choloŵa chakecho chikhale cha abale a bambo wake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngati alibe abale muzipereka cholowa chake kwa abale a abambo ake. |
Ndipo akapanda abale a atate wake, mupatse wa chibale wake woyandikizana naye wa fuko lake cholowa chake, likhale lakelake; ndipo likhale kwa ana a Israele lemba monga Yehova wamuuza Mose.