Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.
Numeri 21:10 - Buku Lopatulika Pamenepo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema mu Oboti. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'Oboti. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Aisraele adanyamukanso, nakamanga mahema ao ku Oboti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Aisraeli anayendabe nakamanga misasa yawo ku Oboti. |
Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.