Ndipo simudzasenzapo uchimo, mutakwezako zokometsetsa zake; ndipo musamaipsa zinthu zopatulika za ana a Israele, kuti mungafe.
Numeri 19:1 - Buku Lopatulika Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anati kwa Mose ndi Aaroni: |
Ndipo simudzasenzapo uchimo, mutakwezako zokometsetsa zake; ndipo musamaipsa zinthu zopatulika za ana a Israele, kuti mungafe.
Ili ndi lemba la chilamulo Yehova adalamulirachi, ndi kuti, Nena ndi ana a Israele kuti azikutengera ng'ombe yaikazi yofiira, yangwiro yopanda chilema, yosamanga m'goli;