Numeri 13:9 - Buku Lopatulika Wa fuko la Benjamini, Paliti mwana wa Rafu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la Benjamini, Paliti mwana wa Rafu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la Benjamini, adatuma Paliti mwana wa Rafu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera ku fuko la Benjamini, Paliti mwana wa Rafu; |
Khalani amphamvu, limbikani mitima, musamachita mantha, kapena kuopsedwa chifukwa cha iwowa; popeza Yehova Mulungu wanu ndiye amene amuka nanu; Iye sadzakusowani, kapena kukusiyani.
Ndipo Yehova, Iye ndiye amene akutsogolera; Iye adzakhala ndi iwe, Iye sadzakusowa kapena kukusiya; usamachita mantha, usamatenga nkhawa.
Musamawaopa; mukumbukire bwino chimene Yehova Mulungu wanu anachitira Farao, ndi Ejipito wonse;
Musamaopa pamaso pao; popeza Yehova Mulungu wanu ali pakati pa inu, Mulungu wamkulu ndi woopsa.