Numeri 13:7 - Buku Lopatulika Wa fuko la Isakara, Igala mwana wa Yosefe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la Isakara, Igala mwana wa Yosefe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la Isakara, adatuma Igala mwana wa Yosefe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera ku fuko la Isakara, Igala mwana wa Yosefe; |
Pamenepo ana a Yosefe ananena ndi Yoswa, ndi kuti, Watipatsiranji cholowa chathu chamaere chimodzi ndi gawo limodzi, popeza ife ndife anthu aunyinji, pakuti Yehova anatidalitsa ndi pano pomwe?