Numeri 13:13 - Buku Lopatulika Wa fuko la Asere, Seturi mwana wa Mikaele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la Asere, Seturi mwana wa Mikaele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la Asere, adatuma Seturi mwana wa Mikaele. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera ku fuko la Aseri, Seturi mwana wa Mikayeli; |
Pamenepo tinayenda ulendo kuchokera ku Horebu, ndi kubzola m'chipululu chachikulu ndi choopsa chija chonse munachionachi, panjira ya ku mapiri a Aamori, monga Yehova Mulungu wathu anatiuza; ndipo tinadza ku Kadesi-Baranea.