Iwo ndiwo oitanidwa a khamu, akalonga a mafuko a makolo ao; ndiwo akulu a zikwizo za Israele.
Numeri 1:17 - Buku Lopatulika Ndipo Mose ndi Aroni anatenga anthu awa, onenedwa maina ao; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose ndi Aroni anatenga anthu awa, onenedwa maina ao; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose ndi Aroni adaŵatenga anthu amene atchulidwaŵa, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mose ndi Aaroni anatenga anthu amene mayina awo anaperekedwa, |
Iwo ndiwo oitanidwa a khamu, akalonga a mafuko a makolo ao; ndiwo akulu a zikwizo za Israele.
nasonkhanitsa khamu lonse tsiku loyamba la mwezi wachiwiri, ndipo iwo anawakumbira magwero ao kutchula mabanja ao, ndi nyumba za makolo ao, ndi kuwerenga maina kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu mmodzimmodzi.
Iyeyu, wapakhomo amtsegulira ndi nkhosa zimva mau ake; ndipo aitana nkhosa za iye yekha maina ao, nazitsogolera kunja.