Nehemiya 7:57 - Buku Lopatulika Ana a akapolo a Solomoni: ana a Sotai, ana a Sofereti, ana a Perida, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a akapolo a Solomoni: ana a Sotai, ana a Sofereti, ana a Perida, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mabanja a antchito ake a Solomoni anali aŵa: a banja la Sotai, a banja la Sofereti, a banja la Perida, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za antchito a Solomoni: Zidzukulu za Sotai, zidzukulu za Sofereti, zidzukulu za Perida |
Awa tsono ndi akulu a dziko okhala mu Yerusalemu; koma m'midzi ya Yuda yense anakhala pa cholowa chake m'midzi mwao, ndiwo Israele, ansembe, ndi Alevi, ndi antchito a m'kachisi, ndi ana a akapolo a Solomoni.