Ana a Bebai, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.
A banja la Bebai 628.
Zidzukulu za Bebai 628
Ana a Bebai, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza awiri.
Ana a Binuyi, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu.
Ana a Azigadi, zikwi ziwiri mphambu mazana atatu kudza makumi awiri ndi awiri.