Ndi a ana a Elamu: Mataniya, Zekariya, ndi Yehiyele, ndi Abidi, ndi Yeremoti, ndi Eliya.
Nehemiya 7:12 - Buku Lopatulika Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa A banja la Elamu 1,254. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za Elamu 1,254 |
Ndi a ana a Elamu: Mataniya, Zekariya, ndi Yehiyele, ndi Abidi, ndi Yeremoti, ndi Eliya.
Ndi wa ana a Elamu, Yesaya mwana wa Ataliya; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu ndi awiri.
Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi limodzi ndi asanu ndi atatu.