Nehemiya 2:11 - Buku Lopatulika Motero ndinafika ku Yerusalemu, ndi kukhalako masiku atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Motero ndinafika ku Yerusalemu, ndi kukhalako masiku atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho ndidafika ku Yerusalemu ndipo ndidakhala kumeneko masiku atatu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndinafika ku Yerusalemu, ndipo ndinakhala kumeneko masiku atatu. |
Ndipo ndinauka usiku, ine ndi amuna owerengeka nane, osauza munthu yense ine choika Mulungu wanga m'mtima mwanga ndichitire Yerusalemu; panalibenso nyama ina nane, koma nyama imene ndinakhalapo.