Hatusi, Sebaniya, Maluki,
Pasuri, Amariya, Malikiya,
Harimu, Meremoti, Obadiya,
wa Maluki, Yonatani; wa Sebaniya, Yosefe;
Amariya, Maluki, Hatusi,
Ndi pambali pao anakonza Yedaya mwana wa Harumafa, pandunji pa nyumba yake. Ndi pambali pake anakonza Hatusi mwana wa Hasabineya.