Koma kuti mudziwe kuti ali nazo mphamvu Mwana wa Munthu pansi pano za kukhululukira machimo (pomwepo ananena kwa wodwalayo), Tanyamuka, nutenge mphasa yako, numuke kunyumba kwako.
Mateyu 9:7 - Buku Lopatulika Ndipo ananyamuka, napita kunyumba kwake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ananyamuka, napita kunyumba kwake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Munthu uja adadzukadi namapita kwao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo munthuyo anayimirira napita kwawo. |
Koma kuti mudziwe kuti ali nazo mphamvu Mwana wa Munthu pansi pano za kukhululukira machimo (pomwepo ananena kwa wodwalayo), Tanyamuka, nutenge mphasa yako, numuke kunyumba kwako.
Ndipo m'mene anthu a makamu anachiona, anaopa, nalemekeza Mulungu, wakupatsa anthu mphamvu yotere.