Ndipo ansembe aakulu anatenga ndalamazo, nati, Sikuloledwa kuziika m'chosonkhera ndalama za Mulungu, chifukwa ndizo mtengo wa mwazi.
Mateyu 27:7 - Buku Lopatulika Koma anapangana, nazigula munda wa woumba mbiya, ukhale manda a alendo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma anapangana, nazigula munda wa woumba mbiya, ukhale manda a alendo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho adapangana kuti ndalamazo agulire munda wa mmisiri wa mbiya, kuti ukhale manda a alendo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho anagwirizana kuti ndalamazo azigwiritse ntchito pogulira munda wa wowumba mbiya kuti ukhale manda alendo. |
Ndipo ansembe aakulu anatenga ndalamazo, nati, Sikuloledwa kuziika m'chosonkhera ndalama za Mulungu, chifukwa ndizo mtengo wa mwazi.