Chotero inunso m'mene mutachita zonse anakulamulirani, nenani, Ife ndife akapolo opanda pake, tangochita zimene tayenera kuzichita.
Luka 17:9 - Buku Lopatulika Kodi ayamika kapoloyo chifukwa anachita zolamulidwa? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kodi ayamika kapoloyo chifukwa anachita zolamulidwa? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kodi ungamthokoze wantchitoyo chifukwa chakuti wachita zimene unamlamula? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kodi iye angathokoze wantchitoyo chifukwa chochita chimene anawuzidwa kuchita? |
Chotero inunso m'mene mutachita zonse anakulamulirani, nenani, Ife ndife akapolo opanda pake, tangochita zimene tayenera kuzichita.
wosanena naye makamaka, Undikonzere chakudya ine, nudzimangire, nunditumikire kufikira ndadya ndi kumwa; ndipo nditatha ine udzadya nudzamwa iwe?