Ndipo panali pamene Iye analowa m'nyumba ya mmodzi wa akulu a Afarisi tsiku la Sabata, kukadya, iwo analikumzonda Iye.
Luka 14:2 - Buku Lopatulika Ndipo onani, panali pamaso pake munthu wambulu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo onani, panali pamaso pake munthu wambulu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pomwepo pamaso pake panali munthu wina wambulu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Poteropo, patsogolo pake panali munthu amene anadwala matenda otupa mimba ndi miyendo. |
Ndipo panali pamene Iye analowa m'nyumba ya mmodzi wa akulu a Afarisi tsiku la Sabata, kukadya, iwo analikumzonda Iye.
Ndipo Yesu anayankha nati kwa achilamulo ndi Afarisi, nanena, Kodi nkuloledwa tsiku la Sabata kuchiritsa, kapena iai?