ndipo Enoki anayendabe ndi Mulungu, atabala Metusela, zaka mazana atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi;
Genesis 5:23 - Buku Lopatulika masiku ake onse a Enoki anali mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi ndi zisanu; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 masiku ake onse a Enoki anali mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi ndi zisanu; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adamwalira ali wa zaka 365. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zaka zonse za Enoki zinali 365. |
ndipo Enoki anayendabe ndi Mulungu, atabala Metusela, zaka mazana atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi;