Genesis 5:12 - Buku Lopatulika Ndipo Kenani anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi awiri, ndipo anabala Mahalalele: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Kenani anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi awiri, ndipo anabala Mahalalele: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kenani ali wa zaka 70, adabereka mwana dzina lake Mahalalele, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Kenani anali ndi zaka 70, anabereka Mahalaleli. |
ndipo Kenani anakhala ndi moyo, atabala Mahalalele zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi anai, ndipo anabala ana aamuna ndi aakazi;
mwana wa Metusela, mwana wa Enoki, mwana wa Yaredi, mwana wa Mahalalele, mwana wa Kainani,