Nati kwa Farao, Tafika kuti tikhale m'dzikomo; popeza palibe podyetsa zoweta za akapolo anu; pakuti njala yakula m'dziko la Kanani. Mulole tsopano akapolo anu akhale m'dziko la Goseni.
Genesis 47:5 - Buku Lopatulika Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Atate wako ndi abale ako afika kwa iwe; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Atate wako ndi abale ako afika kwa iwe; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Farao adauza Yosefe kuti, “Bambo wako pamodzi ndi abale ako abwera kwa iwe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Farao anati kwa Yosefe, “Abambo ako ndi abale ako abwera kwa iwe. |
Nati kwa Farao, Tafika kuti tikhale m'dzikomo; popeza palibe podyetsa zoweta za akapolo anu; pakuti njala yakula m'dziko la Kanani. Mulole tsopano akapolo anu akhale m'dziko la Goseni.
dziko la Ejipito lili pamaso pako: uwakhazike atate wako ndi abale ako pa dera lokometsetsa la dziko; akhale m'dziko la Goseni; ndipo ngati udziwa anthu anzeru a mwa iwo, uwaike iwo ayang'anire ng'ombe zanga.