Ndipo anauka usiku womwewo, natenga akazi ake awiri, ndi adzakazi ake awiri, ndi ana ake aamuna khumi ndi mmodzi, naoloka pa dooko la Yaboki.
Genesis 32:23 - Buku Lopatulika Ndipo anawatenga iwo nawaolotsa pamtsinje, naziolotsa zonse anali nazo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anawatenga iwo nawaolotsa pamtsinje, naziolotsa zonse anali nazo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ataŵaolotsa onse aja, adaolotsanso chuma chake chonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atatha kuwawolotsa pa mtsinjewo anawolotsanso katundu wake yense. |
Ndipo anauka usiku womwewo, natenga akazi ake awiri, ndi adzakazi ake awiri, ndi ana ake aamuna khumi ndi mmodzi, naoloka pa dooko la Yaboki.