ndipo anamuitana Loti, nati kwa iye, Ali kuti anthu amene anadza kwa iwe madzulo ano, utitulutsire iwo kuti tiwadziwe.
Genesis 19:6 - Buku Lopatulika Ndipo Loti anatulukira kwa iwo pakhomo, natseka chambuyo pakhomo pake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Loti anatulukira kwa iwo pakhomo, natseka chambuyo pakhomo pake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Loti adatuluka panja natseka chitseko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Loti anatuluka panja kukakumana nawo natseka chitseko |
ndipo anamuitana Loti, nati kwa iye, Ali kuti anthu amene anadza kwa iwe madzulo ano, utitulutsire iwo kuti tiwadziwe.
Ndipo munthu mwini nyumba anawatulukira nanena nao, Iai, abale anga, musachite choipa chotere; popeza mwamuna uyu walowa m'nyumba mwanga, musachite chopusa ichi.