Ndipo anamanga chapachifuwa pa mphete zake ndi mphete za efodi ndi mkuzi wamadzi, kuti chikhale pa mpango wa efodi, ndi kuti chapachifuwa chisamasuke paefodi; monga Yehova anamuuza Mose.
Eksodo 39:22 - Buku Lopatulika Ndipo anaomba mwinjiro wa efodi, ntchito yoomba ya lamadzi lokha; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anaomba mwinjiro wa efodi, ntchito yoomba ya lamadzi lokha; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adapanga mkanjo wake wa efodi, woombedwa ndi nsalu yobiriŵira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anayipangira efodiyo mkanjo wamtundu wa mtambo, wolukidwa ndi mmisiri waluso. |
Ndipo anamanga chapachifuwa pa mphete zake ndi mphete za efodi ndi mkuzi wamadzi, kuti chikhale pa mpango wa efodi, ndi kuti chapachifuwa chisamasuke paefodi; monga Yehova anamuuza Mose.