Ndi pa mbali ya kumadzulo panali nsalu zotchingira za mikono makumi asanu, nsichi zake khumi, ndi makamwa ake khumi; zokowera za nsichi ndi mitanda yake yasiliva.
Eksodo 38:13 - Buku Lopatulika Ndi pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mikono makumi asanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mikono makumi asanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa mbali inayo yakuvuma panalinso mamita 23. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, inalinso yotalika mamita 23. |
Ndi pa mbali ya kumadzulo panali nsalu zotchingira za mikono makumi asanu, nsichi zake khumi, ndi makamwa ake khumi; zokowera za nsichi ndi mitanda yake yasiliva.
Nsalu zotchingira za pa mbali imodzi ya chipata nza mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu;