Nuzipanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yake iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yake iwiri;
Eksodo 26:20 - Buku Lopatulika ndi pa mbali yake ina ya chihema, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi pa mbali yake ina ya Kachisi, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo kumpoto kwa chihemacho upangenso mafulemu makumi aŵiri, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo mbali yakumpoto ya chihemacho upangenso maferemu makumi awiri. |
Nuzipanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yake iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yake iwiri;