Eksodo 21:25 - Buku Lopatulika kutentha kulipa kutentha, bala kulipa bala, mkwapulo kulipa mkwapulo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 kutentha kulipa kutentha, bala kulipa bala, mkwapulo kulipa mkwapulo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa kutentha ndi moto kulipa kutentha ndi moto, bala kulipa bala, ndipo mkwingwirima kulipa mkwingwirima. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kutentha ndi moto kulipa kutentha ndi moto, bala kulipa bala, mkwingwirima kulipa mkwingwirima. |
Munthu akampanda mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, padiso, nalithudzula, azimlola amuke waufulu chifukwa cha diso lake.
Ndipo diso lanu lisachite chifundo, moyo kulipa moyo, diso kulipa diso, dzino kulipa dzino, dzanja kulipa dzanja, phazi kulipa phazi.