Ndipo Yehova anati kwa iye, Muka, tsika; nukwere iwe ndi Aroni pamodzi ndi iwe; koma ansembe ndi anthu asapyole kukwera kwa Yehova, angawapasule.
Eksodo 19:25 - Buku Lopatulika Pamenepo Mose anawatsikira anthu, nanena nao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo Mose anawatsikira anthu, nanena nao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo Mose adatsikira kwa anthu kuja kukaŵauza zimenezo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Mose anatsika ndi kukawawuza anthuwo. |
Ndipo Yehova anati kwa iye, Muka, tsika; nukwere iwe ndi Aroni pamodzi ndi iwe; koma ansembe ndi anthu asapyole kukwera kwa Yehova, angawapasule.
(ndinalinkuima pakati pa Yehova ndi inu muja, kukulalikirani mau a Yehova; popeza munachita mantha chifukwa cha moto, osakwera m'phirimo) ndi kuti: