Taonani, popeza Yehova anakupatsani Sabata, chifukwa chake tsiku lachisanu ndi chimodzi alikupatsa inu mkate wofikira masiku awiri; khalani yense m'malo mwake munthu asatuluke m'malo mwake tsiku lachisanu ndi chiwiri.
Eksodo 16:30 - Buku Lopatulika Ndipo anthu anapumula tsiku lachisanu ndi chiwiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anthu anapumula tsiku lachisanu ndi chiwiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero anthu sankagwira ntchito pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kotero anthu anapuma tsiku lachisanu ndi chiwiri. |
Taonani, popeza Yehova anakupatsani Sabata, chifukwa chake tsiku lachisanu ndi chimodzi alikupatsa inu mkate wofikira masiku awiri; khalani yense m'malo mwake munthu asatuluke m'malo mwake tsiku lachisanu ndi chiwiri.
Ndipo mbumba ya Israele inautcha dzina lake Mana; ndiwo ngati zipatso zampasa, oyera; powalawa akunga timitanda tosakaniza ndi uchi.
Masiku asanu ndi limodzi azigwira ntchito; koma lachisanu ndi chiwiri ndilo Sabata lakupumula, msonkhano wopatulika; musamagwira ntchito konse; ndilo Sabata la Yehova m'nyumba zanu zonse.