Ndi chikhulupiriro anasiya Ejipito, wosaopa mkwiyo wa mfumu; pakuti anapirira molimbika, monga ngati kuona wosaonekayo.
Eksodo 10:29 - Buku Lopatulika Ndipo Mose anati, Mwanena bwino; sindidzaonanso nkhope yanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose anati, Mwanena bwino; sindidzaonanso nkhope yanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose adayankha kuti, “Monga momwe mwaneneramu, ine sindidzakuwonaninso.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mose anayankha kuti, “Monga momwe mwaneneramu, Ine sindidzaonekeranso pamaso panu.” |
Ndi chikhulupiriro anasiya Ejipito, wosaopa mkwiyo wa mfumu; pakuti anapirira molimbika, monga ngati kuona wosaonekayo.