Danieli 5:24 - Buku Lopatulika Pamenepo nsonga ya dzanja inatumidwa kuchokera pamaso pake, nililembedwa lembali. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo nsonga ya dzanja inatumidwa kuchokera pamaso pake, nililembedwa lembali. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho Iye watumiza dzanja limene lalemba mawu amenewa. |
Nthawi yomweyo zinabuka zala za dzanja la munthu, ndipo zinalemba pandunji pa choikaponyali, pomata pa khoma la chinyumba cha mfumu; ndipo mfumu inaona nsonga yake ya dzanja lidalembalo.