Fano ili tsono, mutu wake unali wagolide wabwino, chifuwa chake ndi manja ake zasiliva, mimba yake ndi chuuno chake zamkuwa,
Danieli 2:33 - Buku Lopatulika miyendo yake yachitsulo, mapazi ake mwina chitsulo mwina dongo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 miyendo yake yachitsulo, mapazi ake mwina chitsulo mwina dongo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Miyendo yake inali yachitsulo, mapazi ake anali achitsulo chosakaniza ndi dongo. |
Fano ili tsono, mutu wake unali wagolide wabwino, chifuwa chake ndi manja ake zasiliva, mimba yake ndi chuuno chake zamkuwa,
Munali chipenyere kufikira mwala unasemedwa popanda manja, umene unagunda fanoli pa mapazi ake okhala chitsulo ndi dongo, nuwaphwanya.