2 Samueli 4:10 - Buku Lopatulika muja munthu wina anandiuza kuti, Onani Saulo wamwalira, ndi kulingalira kuti alikubwera nao uthenga wabwino, ndinamgwira ndi kumupha ku Zikilagi, ndiyo mphotho yake ndinampatsa chifukwa cha uthenga wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 muja munthu wina anandiuza kuti, Onani Saulo wamwalira, ndi kulingalira kuti alikubwera nao uthenga wabwino, ndinamgwira ndi kumupha ku Zikilagi, ndiyo mphotho yake ndinampatsa chifukwa cha uthenga wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa pamene wina adaandiwuza kuti Saulo wamwalira, naganiza kuti wabwera ndi uthenga wabwino, ine ndidamgwira, ndipo ndidamupha ku Zikilagi. Imeneyo idaali mphotho yomwe adalandira chifukwa cha uthenga wakewo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero pamene munthu wina anandiwuza kuti, ‘Sauli wafa’ ndipo ankaganiza kuti wabweretsa nkhani yabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha ku Zikilagi. Iyi inali mphotho imene ndinapereka kwa iyeyo chifukwa cha uthenga wake! |