Ndipo akumzindawo anatuluka, namenyana ndi Yowabu; ndipo adagwapo anthu ena, ndiwo a anyamata a Davide; ndi Uriya Muhiti anafanso.
2 Samueli 11:18 - Buku Lopatulika Pamenepo Yowabu anatumiza munthu nauza Davide zonse za nkhondoyi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo Yowabu anatumiza munthu nauza Davide zonse za nkhondoyi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Zitatero, Yowabu adatuma wamthenga kwa Davide kukamuuza zonse zimene zidachitika kunkhondoko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yowabu anatumiza wamthenga kwa Davide kukafotokoza mwatsatanetsatane za nkhondoyo. |
Ndipo akumzindawo anatuluka, namenyana ndi Yowabu; ndipo adagwapo anthu ena, ndiwo a anyamata a Davide; ndi Uriya Muhiti anafanso.
Nudza mthenga, numfotokozera, kuti, Abwera nayo mitu ya ana a mfumu. Nati iye, Muiunjike miulu iwiri polowera pa chipata kufikira m'mawa.